Ghetto side
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Ghetto side, Victoria Avenue 46, Mzuzu.
24/07/2026
Mmmmmmmm
JHB
Life is becoming increasingly difficult for many people.
Here in the Johannesburg CBD, many foreign nationals say they are living in fear and uncertainty as tensions continue.(ghetto side)
08/07/2026
DZIKO LA GHANA LAKANA KULANDIRA ULENDO WA MSOGOLERI WA DZIKO LA SOUTH AFRICA
Dziko la Ghana lakana pempho la mtsogoleri wa dziko la South Africa, a Cyril Ramaphosa, lofuna kubwera kudzayendera dzikolo, ‘state visit’ mu Chingerezi.
Malingana ndi zomwe yalemba nyumba yofalitsa nkhani ya DW Africa, akuluakulu a boma la Ghana ati kukanaku kwabwera kutsatira ziwawa zokhudzana ndi kuthamangitsidwa kwa anthu akunja (xenophobia) zomwe zikuchitika ku South Africa.
Boma la Ghana lati ulendowu, womwe umayenera kuchitika kumayambiriro kwa mwezi wa August 2026, aukana chifukwa chofuna kupewa mkwiyo wa anthu ndi ziwonetsero kamba koti anthu akadali ndi maganizo okhudzidwa ndi nkhanza zomwe anthu aku South Africa akuchita kwa alendo, choncho iwo ati chitetezo ndi ulemu pa nzika zawo ndikofunika kwambiri kuposa chilichonse.
Pakadali pano dziko la Ghana lapempha boma la South Africa kuti lipeze njira zolimba zothanirana ndi kuukiridwa kwa alendo ndi kutsimikizira chitetezo chawo m’dzikolo, asanakonzere ulendo wina uliwonse mtsogoleri wawo kupita kumayiko ena.
Ghetto side
Yooooo
Eichi🤣🤣🤣🤣🤣
07/07/2026
🤣🤣🤣🤣🤣
Click here to claim your Sponsored Listing.
Telephone
Address
Victoria Avenue 46
Mzuzu