Kuwala Optics

Kuwala Optics

Share

Optical and eye care services. High quality at low cost.

Photos from Kuwala Optics's post 23/07/2026

GULURA MONTH-END PROMOTION

(Up to 08 August)

Timalize stock imeneyi, tibweretsemo ena. Discount phwamwamwa 🥳

Lipirani K49,000 yokha pama glasses ena aliwonse omwe mtengo wake weniweni sukudutsa K69,000 🥳
[All glasses at/below K69,000 are now selling at K49,000 only]

As usual, timaperekanso zinthu izi kwa onse omwe agula ma glasses;
1. Spectacle case
2. Lens cleaner
3. Lens wiper

Ma glasses amakonzedwa pompopompo. Kuyeza maso ndi ulere 😊

[Premium and Executive frames available]

LILONGWE: Opposite National Bank, Area 2.
BLANTYRE: inside Al-amin Arcade, opposite AXA.
AREA 25: Nsungwi, after Matabwa market.

Call/Whatsapp: 0990511960

Photos from Kuwala Optics's post 16/07/2026

CONGRATULATIONS 🎊

Ms Mírríé Úm Magombo and Mr. Jack Tombolombo zatengeni your Kuwala Packages, mwaiphula 🥳



NOTE: The instruction was kuti tinene zimene mnzathu wapakamwa uja anganene atakuonani kuti mwavala Kuwala Package for the first time 😁 Nde some people had more Likes, koma they had not responded to the instruction.

Congrats Mirrie and Jack! 🥳

14/07/2026

KENAKO GULULU

Mwakumanizana naye mnzanu uja, iyeyo samatha kungokhala chete mukavala ka Latest kenakake, kwake nkuiyankhulira basi mene iyeyo waimvelera 😂

Atha kumati chani mutati mwakumana naye for the first time mutavala tima Kuwala Packages iti?

(Price yake timeneti ndi K89,000. Pa 85k zikumatheka)

Best comment with more Likes (1 male, 1 female) wins the Kuwala Package 🥳.
You can tag friends to like your comment (no zigoba accounts)

Remember: All glasses below K69,000 are now selling at K49,000 only 😊

Photos from Kuwala Optics's post 11/07/2026

49K STOCK

Stock iyiyi mtengo wake ndi K49,000 only, ali available in all our shops 😊
Komanso timaperekanso izi kwa amene agula ma glasses;
1. Spectacle case
2. Lens cleaner
3. Lens wiper

Ma glasses amakonzedwa pompopompo 😊 Kuyeza maso ndi ulere.

[Premium and Executive frames available]

LILONGWE: Opposite National Bank, Area 2
BLANTYRE: inside Al-amin Arcade, opposite AXA.
AREA 25: Nsungwi, after Matabwa market.

Call/Whatsapp: 0990511960

Photos from Kuwala Optics's post 05/07/2026

INDEPENDENCE MEGA-PROMOTION

(06 - 11 July)

Tatsitsa mitengo pokondwelera Independence, ma discount mpaka K15,000 😊

As usual, tikuperekabe zinthu iziz mukagula ma glasses;
1. Spectacle case
2. Lens cleaner
3. Lens wiper

Mitengo: K49,000 to K80,000 😊

Kuyeza maso ndi ulere. Ma glasses amakonzedwa pompopompo.

[Premium and Executive frames available]

LILONGWE: Opposite National Bank, Area 2
BLANTYRE: inside Al Amin Arcade, opposite AXA
AREA 25: Nsungwi, after Matabwa market

Call/Whatsapp: 0990511960

05/07/2026

INDEPENDENCE DAY
👓
Open - 08:00 am
Close - 02:30 pm

01/07/2026

AZIBAMBO SET

Iyiyi nde ma gentlemen ambiri imawawaza heavy.
Taibweretsanso mu stock, available in all our shops. Katundu wabwino okhaokha.

K89,000 yokha.

23/06/2026

PROMOTION ILIPOBE

(Mpaka Saturday, 27 June)

Ititi panopa tili pa K65,000 only.

All glasses tikuchotsera K10,000. Pomwe ma glasses a frame ya Transparent tikuchotsera K15,000 😊

Photos from Kuwala Optics's post 15/06/2026

STOCK CLEARANCE

(Up to 27 June)

Discount ya K10,000 pama glasses ena alionse 🥳 Mukagula ma glasses, pompo mumalandiranso zinthu izi;
1. Spectacle case
2. Lens cleaner
3. Lens wiper

Bonus: Mukasankha ma frames a Transparent or White, palinso extra discount ya K5,000 🥳

Mitengo: K49,000 to K89,000

Kuyeza maso ndi ulere. Ma glasses amakonzedwa nthawi yomweyo 😊

[Premium and Executive frames available]

LILONGWE: Opposite National Bank, Area 2.
BLANTYRE: inside Al-amin Arcade, Opposite AXA.
AREA 25: Nsungwi, after Matabwa market.

Call/Whatsapp: 0990511960

Photos from Kuwala Optics's post 08/06/2026

BEAUTIFUL PEOPLE

See good looks 😊

Team iyi yabebha, anazaphulira ma Prizes awo, full Kuwala Packages.

Collie Strings anabwera ku Blantyre shop, pomwe Jayne W Banda anabwera ku Area 25 shop.

Mumakwana guys 🎊

(Price range: K55,000 to K95,000)

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address


Area 2
Lilongwe

Opening Hours

Monday 08:00 - 16:30
Tuesday 08:00 - 16:30
Wednesday 08:00 - 16:30
Thursday 08:00 - 16:30
Friday 08:00 - 16:30
Saturday 08:00 - 14:00