Somo Bridal Store

Somo Bridal Store

Share

Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Somo Bridal Store, Beauty Store, Machinjiri Nthawila, Blantyre.

18/08/2026

goodnyt from our beautiful bride Rachel
ndanena kale dzulo kuti kuno timakhala ndi ma headband komanso ma morning gowns okongola

18/08/2026

Chinthu chija tatenga,. Mkakamkaka
Contact us today and get your service from Somo Bridal Store.

Photos from Somo Bridal Store's post 18/08/2026

Kuno ma dress ndi mpwechepweche, eya ngambwingambwi. Mudzisowa mtendere chifukwa chokanika kusankha 😂.

Photos from Somo Bridal Store's post 18/08/2026

kuno nde kwacha boh ,,,,,Ka kumeneko????
osaiwala kuti kuno tili ndimadress okongola

0988449160

17/08/2026

Promotion yomwe inatetha lero, zonsezi ndi ife a Somo Bridal Store.Mukhale ndi usiku opambana Akasi.

Photos from Somo Bridal Store's post 17/08/2026

Apa kuwala, apo kuwala , ona kuwalaa, ma set a clean ndifeyo a Somo Bridal Store. Mkakamkaka, we make your wedding memorable. Faka like and share iwe 🩷.

Photos from Somo Bridal Store's post 17/08/2026

Akasi Dress la k280 pin apa likupita pa k140. Atatu achangu contact us on WhatsApp muwale. Kaya tsiku lanu likuyenda bwanji?

wa.me/0988449160.
Somo Bridal Store

Photos from Somo Bridal Store's post 17/08/2026

Kadzutsa, Ona kuwala kwa bride wathu!!. Apatseni like tiwone.

16/08/2026

Kodi akasi madziwanso kuti timakhala ndima Headband ama bride?..Zonsezi kuti Inu muwale.

16/08/2026

umaziwa umaziwa

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address


Machinjiri Nthawila
Blantyre