Health tips
Wash up your body twice a day
14/06/2026
20/03/2026
*LONG LASTING MALE SPRAY*
aaaaaasa
Azibambo ambiriwa, or atatchena ambiriwa akukumana ndi vuto la eary ej*******on.
Eary ej*******on ikuchitika pa zifukwa zambiri
Kulera wa mayi,
Ma stress
Ma infections
Zakudya/zakumwa ndi zina Zambiri.
Nde ikakwana nthawi ya bwandulebwandule, kungogundisa nthawi yomwe malume fwaaaa.
Pamenepo mayi watetha ready kuti ayambe kuwakha ma penalty, bambo yambani, bambo ali ine ndamaliza kale.
Mayi akatero amangomezela mkhawa Ku mtima.
Izi zikamapitilira akudyerani ena muona ohhh.
Komano on a serious note vuto losachedwa kumathirali, azibambo ambiri nde akukumana nalo pa zifukwa zomwe ndanenazo. Nde kuti muthane ndi ma 20 seconds anuwo, yankho ndi male spray. Inu abale enatu or 1 minute samafika.
Male spray uyuyu umangomfaila Gadafiyo 20 mins before game. Zikatero uyo wadxuka kulilira ngati mkango. Nde umamugwila bwino ntchito mwana wayini ake kuti nayeso ayiwale njira ya kwawo. Aaaa osati kungoti gu nthawi yomwe fwaaaa.
Tagulani long lasting male spray
DESTINY HERBAL PRODUCTS
0885777241/0997088677
27/01/2026
Zizindikiro za mauka ni monga:
- *Kumva kuyabwa ku maliseche*
- *Kufiira kwa kumaliseche*
- *Kutuluka madzi kapena chikazi chochuluka komanso cha fungo*
- *Kumva kutentha komanso kupweteka kumaliseche*
- *Kumva ululu mkazi akangomaliza kugonana ndi mamuna olo kapena ululu akangomaliza kukodza*
- *Kutuluka tinsungu olo zilonda kumaliseche a mwamuna*
Zomwe zimayambisa mauka ni:
- *Bacteria or fungi*
- *Nyongolosi za mumatumbo*
- *Kuchepa kwa vitamin b nthupi*
- *Mankhwala (chemicals)*
- *Zopaka paka ndi kupopera mu pheche mpeche olo nthupi*
- *Kuvala zovala zothina kwambiri monga ma panti*
- *Kuvala zinthu zokuda komanso zonyowa monga mapanti*
- *Umve wa mkati*
- *Nthenda ya shuga komanso ma antibiotics*
- *Kusavala ma panti monga kwa inu adzimayi idzi zimapangisa kuti fumbi lidzilowa ku ndata kwanu*
- *Mankhwala ena*
- *Adzimai ena amatha kukhala ndi mauka chifukwa choti ngoyembekedzera*
- *Zakudya zomwe zili ndi shuga kwambiri*
- *Zokumwa zoledzeretsa*
- *Kugonana mosadzitetedza*
Ipa pali zipangizo zomwe zingakuthandizeni kupewa mauka:
๐ฏ Mukamaliza kugonana musavaleso pant๐ unless maliseche muwonetsetse kuti awuma and mwatsuka.
๐ฏ Musamakonde kuvala zonyowa.
๐ฏ Musamavale pant๐ mmodzi modzi.
๐ฏ Nthawi zina ma pant anu muzichapako ndimadzi otentha or muziyanika padzuwa osamangoyanika pamthuzi.
๐ฏ Ngati mulindivuto losachedwa kutuluka madzi kundata ngati mukuyenda muzivalira nyanda pant wanu๐.
๐ฏ Mukamaliza kukodza muziwonetsetsa mwadzipuputa mikodzo yotsalirayo phuzilani kuyenda ndi tissue mu hand bag๐yanu osamangodziwa kusungila face powder ๐.
๐ฏ Mukamapita kosamba muzichapilatu pant ndikukayanika then kuvala wina osamasungila kuti mudzachape akada mapanti ambiri.
Mukusowa mtendere ndi mauka, bwerani ku inbox ya _DESTINY HERBAL AND BEAUTY PRODUCTS_ tili ndi mankhwala othetseratu matenda amenewa ndikuyambaso kukhara moyo wantendere osati omangodandaula ayi. Tipezeni kuno ku _DESTINY HERBAL AND BEAUTY PRODUCTS_ ngati muli kutali timatumiza ndipo mankhwala adzakupezani mosavuta 0885777241/0997088677.
Kuna ndani amene ali ndi swali kapena amafuna kuziwa zambiri pa mauka?
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Telephone
Website
Address
Nyamambadewe
Blantyre