MR 3 B
LOVE CONNECTOR AND OTHER GOOD STORIES wapp me on +265888545597
Morning 3b wadzka bwanji munthune maganizo akumandibalalitsa nkhan yanga ndiyotere ndinalipabanja koma linatha now four yrs and ndimkadzinamiza k*t sindizafunaso mamuna koma zinandikanika and ndinapeza mamunA ondimvesetsa chifukwa munthune kubereka kwanga ndimabereka through cissor apa ananditseka ndilindi ana awir so mamuna uyu anavomereza k*t tilera omwe alipowa ndiomwe mkaz wake anasiya ndimamuna wabwno okonda komaso omvesetsa koma ndi contractor ot sangakhaleso pakhomo ndi always MMA field zomwe mtima wanga sukukondwa ndikusowa chikondi Chamamuna munthune mwana wanga oyamba Ali kuschool omaliza bamboo Ake anatenga bas ndekha ndekha Moyo kuwawa kwambir now ndimafuna munthu oti ndizicheza naye oti amakhala ekha around Dedza Ntcheu balaka kot nditha kupita kukacheza masiku angapo sinkhan yandalama ai akapanga provide transport pazikhala pakwana am 34yrs old chubby
Amene aumufuna mkaziyu andipeze pa 0888545597
Mwamuba waboma lililonse Kaya BT Lcity Balaka etc etc iye ali Ntcheu onenepa bhoooo
Tiyeni titolane
Titati titolane mu page muno, inuyo mungatole ndani ???
Ofanana or osiyana gender tolanani
Mumpange tag aziwe k*ti mumafira
Akane yekha bola chilungamo achiziwe
Agayireni amnzanu 2000 kwacha angokupa kaphala mvulayi sakwanisa kukasaka maganyu
Lemba mawu oti K2000
Wachifundo akupasa koma osasunga # yake k*ti mawa muzamupemphenso choncho sibwino
Koma mvula imeneyi ati nchani abale
Makala ndikaufa kokupha phala muli nazo koma ????
Morning
Iney ineed a boyfriend woti tizimvana kmaso azindithandiza some stuffs like groceries sometimes rent akhale wachochita kmaso akhale oti alibe girl wina iwant to be in a relationship ican be alone zopanga share mamuna ndi akaz enaosawaziwa zandikwana please only serious men for serious relationship age between 23 to 28
Soche or long distance relationship bhobho as long as the man be able kt tizikumana though after long time
Kantsikana ka bho kokongola kalibe mwana kasukulu yake
Akufuna mwamuna wachibwenzi wantsinkhu wake osakwana zaka 30
Waboma lililonse bola azikwanisa kumuyendera or kumuitanisa
Ndipezeni men pa 0888545597
Kanyengo kameneka muli awiri
Zokomatu
Mumufuna okugonesani ?????
Ndimafuna mundithokozere ku group Kwa sister Salome Kamanga omwe anandipempha number yanga,ndipo andigaila ndlama yokwana k2000 ,yafika ndithu ambuye awadalitse,ine Happiness zikomo
Hy pls ngati zingatheke ndipangileko post ku group mwana wanga wadwala maso MOTi atupa sakuona akamalila akumatuluka ma**ga***zi chonde athu ku group andithandize ndalama yamakhwala
Kodi muli singo be
Are you still single ???
????
Eya
Ai
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
BLANTYRE
Blantyre
Alerts
Be the first to know and let us send you an email when MR 3 B posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.