Blessed Herbals
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Blessed Herbals, Health/Beauty, Blantyre.
11/09/2026
🦠KWA OKHAWO AMENE🦠 ANAPEZEKA NDI MATENDA A HIV 🧬and AIDS🧬🧬
🦠KODI MULI NDI ENA MWA MAFUSO AWA?! 🦠
🦠Kodi ndizakhala chonchi mpaka liti?
🦠Kodi nditasiya kumwa mankhwalawa chingachitike ndi chani ku moyo wanga?
🦠Ndizinthu ziti zimene zingandithandize kuti ndizikhaka ndi moyo wathanzi ngakhale ndili ndi vutoli?
🦠Ndi zinthu ziti zimene sindikuyenela kuchita nawo, kudya nawo zomwe anthu amene alibe vutoli amapanga?
🦠Ndingatani kuti ndisapatsile anthu amene andizungulira komaso okondedwa anga?
🦠Kodi nditafuna kubeleka, sindingapatsile mwana wanga vutoli?
🦠Kodi ndi zotsatila zabwino ndi zoipa ziti zimene ndingayembekezele chifukwa Cha mankhwala ndikumwawa?
🦠Kodi Ndingatani kuti ndi ndithane nalo vuto limeneli pa moyo wanga?
🦠Kodi ndikuyenela kuti ndizikhala odandaula ndi osasangalala nthawi zonse chifukwa Cha vuto langali?
🦠Nditani naye munthu uja anandipatsa matendawa? Ndidane naye kapena ndivomeleze kuti nayeso sikunali kufuna kutengela?
🦠Kodi mchifukwa chiyani anthu amene anabadwa Ali positive akhala akumwa mankhwala kwanthawi Yaitali sasinthika thupi maonekedwe, nkhope, mikoni ndi miyendo or mimba pamene anthu amene tapezeka nayo titakula kale nkhope zathu, mimba zathu, miyendo yathu, kaonekedwe Kathu kakusinthika chonchi?
🦠Kodi popeza ndili kutali ndipo mankhwala sindikumwa, ondilandilira or ondibweletsela palibe, Ndingatani kuti ndikhalebe ndi moyo wanthazi ndi wamphavu?
NGATI MMAKHALUPILIRA KUTI MULUNGU AMACHIZA NDIPO ANGATHE KUTHANA NDI VUTO LANU, NDIPO PALIBE NTHANDA YOSACHIZIKIZA, MUNAVAPOSO KUTI ENA ANAKHALA BWINO ATAKHALA NDI VUTO NGATI LANULO, NANUSO NDIZOTHEKA.
Simukuyenela kumadandaula ndi vuto lanu kwambiri chifukwa mmene ikuzuzila anthu BP ndi Sugar, mukanakhala pansi ndikuyamika kuti Ambuye mwandikondela, sindikuyenela kumadandaulaso.
Ngati muli ndi mafuso awo ndipo mulinacho chidwi chodziwa ndikuphuzila zambiri ngakhaleso kupeza nthandizo kumene Tilankhulane
WHATSAPP 0995506376
11/09/2026
THE FORBIDDEN BOOK OF ENOCH part 6(last part)
Lero timalize nkhani yathu yomwe inayambira mu book la Enoch lomwe silinaikidwe mu bible.ndiye mwina ena mwaiwala komwe yachokera nkhani imeneyi ya ma Alien.
Ndiye mongokumbutsana,tinanena kuti angelo omwe anaikidwa kuti aziyang'anira anthu,anayamba kusilira akazi a padziko pano mpakana nkugona nawo ndipo ana omwe akaziwa amabereka amakhala osiyana kwambiri ndi munthu olengedwa ndi Mulungu.chitsanzo chabwino ndi Goliat.
Mulungu atawona zonyasa zomwe angelowa anachita,Iye anatumiza angelo ake a mphamvu omwe anagonjetsa ma fallen angel onse 200 ndikuwaponya ku chidzenje cha mdima komwe akudikilira tsiku la chiweruzo.
Kenako Mulungu anawononga zamoyo zonse pogwiritsa ntchito mvula ndipo linapulumuka ndi banja la Nowa basi.
Mizimu ya ana angelo aja ndi yomwe lero tikuti ziwanda ndipo ma demon amenewa ali m'manja mwa Lucifer.
Ndiye chomwe tikunena pano ndichakuti America inapanga ubale ndi angelowa ndipo ayamba kupanga ma aliens omwe adzawatulutse bwinobwino ukadzangochitika mkwatulo.
Akhristu enieni akazangokwatulidwa,anthu ambiri adzakhala ndi mafunso opanda mayankho ndipo ena azidzafuna kuti adziwe komwe abale awo ali.pamenepa, akatswiri aku America,adzatengerapo mwayi wowanamiza anthu kuti zianthu zochokera kumwamba ndi zomwe zatenga anthu osowawo(Alien invasion)
Okhawo omwe anaphunzitsidwa za mkwatulo ndi omwe adzadziwe choona chenicheni
Plan imeneyi inayambira patali chifukwa padakali pano,apanga Kale ma alien spaceship omwe azidzauluka mlengalenga ndicholinga choti aliyense azakhulupilire bodza lawolo.ndiye ntchito yoseyi ikuchitikira ku area 51 dela lotchedwa Nevada.
Tinanena Kale mbuyomu kuti Malo amenewa ndi achinsinsi kwambiri moti palibe amene amadziwa chomwe chimachitika kumeneko.
Olo president waku America samadziwa ma project onse omwe akuchitika ku area 51.ngakhale zisankho zaku America zambuyomu,Hillary Clinton analonjeza kuti akazangowina,adzapanga kafukufuku waku area 51 ndicholinga choti aliyense adziwe chenicheni chomwe chimachitika kumeneko.
Komamso Kwa amene simukudziwa,ku dela lina la mdziko la America,kunagwa chinthu china chosadziwika chomwe chinali ndimapiko ngati ngelo.
Anthu ambiri anali ndi chidwi ndi chinthucho ndipo amafuna kudziwa komwe chinachokera koma akuluakulu a boma la America anangoipondereza nkhaniyo mpakana pano anthu samadziwa chilungamo cha chenicheni.chimunthu chimenechi ndi chimodzi mwa zinthu zomwe zikupangidwa ku area 51 pogwititsa ntchito nzeru zochokera ku Antarctica komwe kuli ma fallen angels ndipo anachigwetsera dala kuti anthu aziti chachoka kumwamba.
Chinthu china chomwe mungadziwe ndichakuti anthuwa akukonzekera nkhondo ya padziko lonse yachitatu yomwe iyambe posachedwapa.
America ikupanga mfuti zosaphonya komanso asilikali a mphamvu omwe samaphonya powombera mfuti komanso samafa akawomberedwa.asilikali amenewa akupangidwa pogwiritsa ntchito magazi ama fallen angel.zinthuzi zitha kukhala zosakhulupirika lero koma tsiku lina mudzavomerezana nazo.
Pomaliza penipeni tiwoneko chifukwa chomwe bukhu la Enoch silinaikidwe mu Bible.
Bukhuli litapezedwa ndikuwerengedwa,anthu ena sanasangalale nalo ati chifukwa choti limanena zinthu zina mosinjilira kwambiri. Mwachitsanzo,bukhuli limati Enoch amatha kuwerenga nyenyezi zonse zamulengalenga pomwe Bible limati ndi Mulungu yekha amene angathe kuwerenga nyenyezi.kwaineyo sindikudziwa ngati Enoch amadziwadi nyenyezi zonse komano panthawi yomwe ndimawerenga bukhuli ndinapeza kuti Enoch anayenderedwapo ndi ngelo wotchedwa Uliel yemwe anamuphunzitsa zonse Zokhuzana ndi nyenyezi.
Chinanso ndichoti ma Jews ataliwerenga bukhuli, anakana kuti liikidwe mu Bible ati chifukwa choti limavumbulutsa zinsinsi zambiri za kumwamba.mwa njira ina,Iwo samafuna kuti anthu azidziwa zinthu zikuluzikulu zokhuzana ndi kumwamba monga maudindo aangelo.
Izo ndi zina mwa zinthu zomwe zinapangitsa kuti bukhu la Enoch likanidwe ndi Anthu..
Ngakhale mu Bible mulibe mabukhu ena,ilo ndilokwanira kupulumutsa munthu ndipo mawu onse omwe ali mu Bible ndi mpweya wa Mulungu.
Nkhani imeneyi,tiyisiyire Kaye p***a koma idzabweranso ndicholinga choti tizamve zambiri zomwe zikubwera kutsogoloku.
Pomaliza ndikufuna ndikukumbutseni chinthu ichi: Yesu Nkhristu anafunsidwa funso loti,KODI TIZADZIWA BWANJI KUTI TILI M'MASIKU OMALIZA?
Ndipo Yesu anati,masiku amenewa adzakhala ngati a Nowa.ndi chimodzi imodzi kunena kuti zomwe zinkachitika nthawi ya Nowa ndizomwenso zikuyenera kuchitika masiku ano.ndiye ambiri tikamva za mawuwa timangoganiza za mowa,chigololo ndi machimo ena omwe ankachitika nthawi imeneyo koma musaiwale kuti nthawi ya Nowa kunalinso zianthu zoopsa zosadziwika bwinobwino(giants/Nephilims)
M'badwo wodabwitsawu unabwera chifukwa choti angelo anakwatira anthu padziko lapansi.m***a kuwona kuti sizikusiyana ndi zomwe talongotsola mu nkhani yathuyi chifukwa America ikupanga zinthu zosadziwika bwino pogwiritsa ntchito magazi ama fallen angels
Choncho ngati Mukawona ngati zinthu zili bwino padzikoli,dzukani mwachangu ndikudzindikira kuti chimaliziro chafika ndipo Mwana wa Mulungu Yesu Nkhristu akubwera posachedwa.
Be Blessed Herbals
Next story: KODI MPINGO WOLONDOLA NDI UTI?
Ndizaulula
NDIZAULULA ORIGINAL GROUP
04/06/2026
HOSPITALS ARE KILLING YOU. GOING TO ONE MIGHT BE THE WORST DECISION OF YOUR LIFE.
Medical errors are the third leading cause of death worldwide. The system hides the data. Doctors protect each other. And patients go home with infections, wrong-site surgeries, and missed diagnoses. It is time someone said it.
Let me tell you something that will make you sick.
You trust hospitals. You believe that when you walk through those doors, everyone is working to keep you safe. You believe the white coat means competence. You believe the system is designed to protect you.
You are wrong.
Hospitals are dangerous places. Not because the people are evil. Because the system is broken. Because doctors and nurses are overworked. Because they are human. And because there is a culture of silence that protects medical professionals while patients die.
Medical errors are the third leading cause of death in many countries. Not heart disease. Not cancer. Not COVID.
The system itself.
It is killing you. And there is very little accountability.
A landmark study by Johns Hopkins researchers estimated that more than 250,000 deaths per year in the United States are caused by medical error . That makes it the third leading cause of death after heart disease and cancer .
Let that sink in. A quarter of a million people. Every year. Killed by the system that promised to heal them.
And those are only the deaths. The number of patients seriously harmed by medical error – disabled, disfigured, traumatized – is estimated to be 10 to 20 times higher .
Malawi/Zambia does not have good data. But there is no reason to believe the situation is better here. Fewer resources. More overcrowding. Less training. Fewer safeguards.
If anything, the numbers here are worse.
The errors the system hides from you.
Wrong site surgery: Operating on the wrong leg. Removing the wrong kidney. Drilling into the wrong side of the skull. It happens thousands of times a year worldwide. Hospitals call it a "never event" – something that should never happen. Then it happens. And they blame the individual instead of fixing the system.
Missed diagnoses: You come in with chest pain. They send you home with "anxiety." You die of a heart attack three days later. You come in with a headache. They send you home with "migraine." You have a brain bleed. Missed diagnoses are the most common medical error. They happen every day. In every hospital.
Medication errors: You get the wrong drug. The wrong dose. The wrong route. The wrong patient. A nurse gives you insulin meant for the patient in the next bed. A pharmacist misreads a prescription. A doctor prescribes a drug you are allergic to. These happen so often they have stopped counting.
Hospital acquired infections: You come in for a routine procedure. You leave with a superbug. Sepsis. Organ failure. Death. Hospitals call these "complications." You call them what they are: infections they gave you because someone did not wash their hands.
Bedsores: You cannot move. They do not turn you. Your skin breaks down. The wound goes to bone. You get sepsis. You die. From a bedsore. In 2026. This is not medieval history. This is happening right now.
The cover-up is worse than the error.
When a mistake happens, the first instinct is not to tell the patient. It is to hide it. To blame someone else. To blame the patient. To blame the system. To bury the evidence.
Studies show that only a fraction of medical errors are ever disclosed to patients. The justification is protecting patients from distress. But the real reason is protecting the institution from lawsuits.
The result: patients never know what happened. They never get an apology. They never get compensation. They never get justice. And the system never changes.
A 2016 study found that only 11% of harmful medical errors were disclosed to patients in full. Most patients were told nothing. Many were actively misled.
That is not medicine. That is a conspiracy of silence.
The excuses the system hides behind.
"Doctors are overworked."
True. Burnout is real. Staffing is inadequate. But overwork does not excuse killing patients. If an airline pilot is overworked and crashes the plane, society does not say "understandable." It says "negligent."
"Medicine is complex."
True. The human body is complicated. But complexity is not an excuse for wrong-site surgery. Complexity is not an excuse for giving the wrong drug. Some errors are understandable. Most are not.
"Patients are sicker now."
True. But sicker patients require more caution, not less. "Sicker" cannot be an excuse for "worse care."
"Mistakes happen."
They do. But when mistakes happen in any other industry – aviation, nuclear power, manufacturing – the industry investigates, changes systems, and makes sure it never happens again. Healthcare investigates, blames the individual, and waits for the next mistake.
The pushback you will hear:
"This article will make patients afraid to seek care."
Good. They should be cautious. Not afraid. But cautious. Informed. Questioning. The opposite of blind trust. Patients who ask questions get better care. Patients who trust blindly get hidden errors.
"You are attacking doctors."
Yes. Because silence is complicity. Errors happen. Cover-ups happen. Patients are harmed. And the system protects itself instead of protecting patients. That needs to be exposed.
"Not all hospitals are like this."
True. Some are better. Some are worse. But no hospital is perfect. And the culture of silence is everywhere.
"This will cause lawsuits."
Good. Lawsuits are one of the only things that force change. If the threat of litigation is what it takes to make hospitals safer, then sue.
A direct word to every patient reading this:
You have been told your whole life that doctors are heroes. That hospitals are safe. That the system will protect you.
That is a lie.
Doctors are human. They make mistakes. The system hides those mistakes. Professionals protect each other. And you are the one who pays the price.
You do not need to fear doctors. But you do need to watch them. Question them. Hold them accountable.
Your health belongs to you. Not to them.
Act like it.
19/04/2026
Ambiri mpoloni mukuwuziwa .mtengo uwu osapanga nao chibwana the most holie holiest three paziko pano . Vuto lina lililonse lomwe mulinalo osavutika kupita kwa asinganga ayi .
Kaya mufuna kuwina mulandu kapena malo omwe mwagula inu pakuchuluka zitopotopo kungopeza mtengo umeneu kuwuwuza zochota umanva this is the tree that connect you with God directly trust muli pachiphinjo muli pamavuto olo familly yanu ili pachipopsezo chachikulu mwakhala mukulonjezedwa zosiana siyana kaupezeni mtengo wa mpoloni you will get your answers instantly or through your dreams.mtengo okongola muntima uwu olo pachiopsezo chotani mtengo uwu ndichipha mtima olo njoka singakulumeni ataa
Nyumba mwanu mukuchitika zaufiti zosiaya siyana olo mwagula malo omwe pali makangano oti m***a kuluza moyo kaupezeni mtengo wampoloni.mfiti ndi mtengo uwuu nde kutali tali
Munali munthu oyipa mwapanga nyasi ne mtima wanu ukungosowa mtendere olo kufuna kuzimangilira kumene kaupezeni ntengo wampoloni
Kaya busness imene Kaya ndipa company mwakwezedwa udindo nde muli ndi Mantha kaupezen mtengo umeneu
It has so many spiritual aspects titha kuchezere panopa kufotokoza za mtengo wampoloni.God gave us everything we need through the power of nature koma anthu sitiziwa ayi.
Inuo kungosamba mpoloni nothing can shake your life zilipo zinthu zitatu zomwe timasakaniza when it comes to cleansing tibwera nao topic
Omwe muli ndi mtengo uwu your blessed ndipo osadula uchengeteni komanso ngat mwakumana ndi post iyi ndinu odala, omwe mungaufune Whatsapp 0888213553.
Zikomo!
30/03/2026
Munamvapo Zotani Zokhuza Black Seeds? nanga Red ♥️ Jatropha??
Zoti zimalimbana ndi kugonjesa matenda, tizilombo/mavayilasi mumaziwa???
Akuti kuli matenda opanda makhwala? Mmmmh inu ganizaniso kawiri, pano za Corona-Vayilasi mene inathera Boma linafotokoza ngati? Komatu amati Corona nayo yabwera kuzakhala ilibe makhwala, Komanso HIV ndi Corona or Ebola zoopya ndi zinazi...
So why HIV yokha ndi yomwe imangokambidwa Kwa nthawi yayitali... Koma Ili yosaopya ngati Corona or Ebola?
Boma limapeza ndalama, zithandizo kuchoka kunja mu dzina la HIV, anthu ena ochuluka analembedwa ntchito mu dzina la HIV ndiye kuti avomereze kuti imatha kutha samafuna dala...
Inuyo mumakhulupilila kuti MULUNGU ndi wa mphabvu ndipo palibe chomlaka, koma ikafika nkhani ya HIV ndiye munachivomereza kuti basi ndiyamyaya ilibe makhwala or singathe??
Munamvapo za ma herbs a BSM opangidwa ndi a Blessed Herbals ?
ma herbs awa mumasakanizidwa ma ingredients odusa 10, kuphatikiza Black Seeds, Red Jatropha, Cinnamon, Neem, Moringa etc...
Zomwe zili zampabvu pogonjesa matenda, kupha tizilombo, mavayilasi, ma bacteria 🦠 etc...
Komanso m***a kumwa ma herbs Amenewa or musakudwala pongofuna kungopanga service thupi, kusuka magazi, kuchengetera umoyo...
Imbani 0888213553 or Whatsapp kuti muve zambiri, mupeze nawo or muwapezere achibale or azanu ma herbs Amenewa...
Zikomo!
03/02/2026
💊💊🦠ZOTSATILA ZOGWILITSA 💊NTCHITO MA ARVS💊🦠 KWA NTHAWI YAITALI 🦠💊💊🦠💊
🦠Pamwamba pa kutalikitsa moyo ndikuchepetsa chiopsezo chopatsila anthu ena matenda a HIV, palibeso ubwino wina umene umanene kuposela kuipa kwake, tiyeni tikhalire limodzi.
🦠💊Amapangitsa kagawikidwe ka mafuta mthupi kukhala kosiyana(Lipodystrophy syndrome)
🦠💊Amapangitsa kuti mafuta achoke mmiyendo ndi mmanja(Lipoatrophy)
🦠💊Amapangitsa kuti mafuta amene achoka kumiyendo ndi mmanja adzazane pa mimba, mmusi mwa khosi, mmikono ndimu ntchafu(Lipohypertrophy)
🦠💊Amabweletsa mavuto a mafupa(osteoporosis)
🦠💊Amapangitsa abambo kukula mabele(Gynecostia)
🦠💊Amasokoneza ubongo kupangitsa munthu kumakhala Ngati mutu wake sugwila bwino
🦠💊Amayambitsaso stroke pamene awononga Spinal cord ndi ubongo
🦠💊Amabweletsa mavuto oiwalaiwala
🦠💊Amasinthitsa kakhalidwe, ma mood swigs osaneneka
🦠💊Amathandizila odwala kumakhala ndi nkhawa komaso opanikizika malingaliro.
🦠💊Amapangidwa odwala kukhala munthu osakhazikika pa zimene akupanga
🦠💊Amabweletsa matenda a sugar, kusaugwila bwino kwa liver komaso ma kidneys
🦠💊Amabweletsa vuto lokanika kugona
🦠💊Amathandizila odwala kukhala mmoyo ozisankha, ozipatula ndi osasangalala mmagulu amzake.
🦠💊Amaononga mitsempha zimene zimapangitsa kumava kutentha miyendo ndi mapazi ngakhaleso dzazi losatha.
🦠💊Amadetsa nkhungu Maka muzikope za diso komaso mmusi mwa diso
🦠💊Amabweletsaso vuto la kusokonekela kwama hormones zimene zimathaso kukhudza ubeleki wa Mai komaso zotupa za kumazila, mkati ndi kunja kwa chibelekero.
🦠💊Amasinthitsa kaonekedwe ka thupi, khope imaphwangika, miyendo imaphwanyika, manja amaphwanyika koma mimba, khosi ndi mapewa zimananala.
NB: Si aliyese amene akugwilitsa ntchito ma arvs angaone mavuto awa, amasiyana thupi ndi thupi ndipo wina akhoza kukhala mavuto ochepa kuyelekeza ndi wina.
🧬Kupanga masewelo olimbitsa thupi, kumadya zakudya zamagulu onse, komaso uphungu ndi upangila wakakhalidwe ndizina zomwe zimathandizilakobe kuti mavuto awa asabwele kwa amene akhudzika ndi mavutowa.
🥦 Pogwilitsa ntchito mankhwala opangidwa kuchokela ku chilengedwe amene amakhala ndi zowayeneleza zothanilana ndi mafuta amene aundikana Malo amodzi, mitsempha yaonongeka, ziwalo sizikugwila bwino ntchito ndi kuthana ndi mavuto ena onse amene abwela chifukwa Cha mavutowa ndizo njira zomwe zimagwilitsidwa ntchito pothanilana ndi mavutowa.
Nkhani yabwino ndi yokuti ife a Blessed Herbals tili ndi ma herbs othana ndi ma virus, kuchosa maside effects a ma ARVs... 0888213553
20/10/2025
🍅 Tomato mukuwonayu ali ndi poison owopysa kwambiri.
Za white zomwe zamelazo ndi fungus (Aspergillus flavus ndi A. parasiticus). Ndipo dziwani kuti fungus ameneyu amatulutsa poison owopysa otchedwa aflatoxin. Aflatoxin ameneyu amawononga thupi pang'ono pang'ono. Pakupita kwa nthawi, amawononga chiwindi ndi kuyambitsa khansa ya chiwindi.
Zilibe ntchito kuti kaya mudula powolapo nkutaya, kaya mutsuka, kaya mumubwatitsa kwambiri, fungus yo samafa ndipo samachokamo.
Blessed Herbals - 0995 50 63 76
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Telephone
Website
Address
Blantyre
Alerts
Be the first to know and let us send you an email when Blessed Herbals posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.