Ungwazi

Ungwazi

Share

Nasanganya wazinthu
kuchimpwilikiti
kumpanipani kwenikweni

Photos from Ungwazi's post 10/09/2026

Sad news๐Ÿ’”

Ku South Africa dera la George Munthu wamwalilira kuganyu anamuyitana ganyu azinzake akuti amakumba pipe then kenako analowa kuti a kiline pipe yo then nthaka inasweka nkuwakwirila wina mutu umawoneka koma agondwewa anali pansi panthaka ndiye zinavuta kuti awapulumutse ndimmene wafera mzathuyi

Mzimu wa Victor Gondwe ukause mtendere๐Ÿ’”๐Ÿ•Š

29/08/2026

Kodi ukuso mukuwelenga ma weeding dress?
Congratulations Onesmus

25/08/2026

A President a ku USA Donald Trump, wati mbendela ya US isitsidwe ku US kwa one week popeleka ulemu kwa Dolly Parton, yemwe wamwalira lero ali ndi dzaka 80. Mzimu wake ukause mtendere๐Ÿ’”
Anayimba nyimbo ya
It's too late
Coat of my colors
Silver and gold
Think of Love
Jolene
Ndinyimbo zambiri๐Ÿ’•๐Ÿ’•

Photos from Ungwazi's post 21/08/2026

Ndiangati omwe sitimaziwa kuti alindimwana wasize yimeneyi?
Happy happy blessed birthday to Ovilera Longwe
๐Ÿ’•๐Ÿ’•



Follow Ungwazi

20/08/2026

Mwana wa 8 years kucapetown wazipha ndichingwe cha pajama (chovala chogonera) chomwe waziphera sichikuziwika mwana wanzathu wakuMalawi Ambuye atonthoze makolo ake๐Ÿ’”๐Ÿ’”



Follow Ungwazi for more news

18/08/2026

Ataluza ma vote ahonorable akuzambia anaganiza zokachotsa denga lomwe lili theka landalama zawo๐Ÿ˜๐Ÿ˜



Follow Ungwazi for more

15/08/2026

Ana onse kulakwa pa school vuto ndi ana mwina aziphunzitsi?


Follow Ungwazi

15/08/2026

British man baby dadie wa Vanesa Pink anapita ku court zitapezeka kuti Mwana amene adali naye siwake after ma DNA asisi athu anamukoloweka British man ๐Ÿ™Œ๐Ÿพ



Follow Ungwazi for more

Mbolanso Bwanji

12/08/2026

Kumayamikirana abale paubale wawo kuyinyamula Malawi ๐Ÿ™Œ๐Ÿพ
akutinyamura abale ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ




Follow Ungwazi for more

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Mzimba?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address

.. .
Mzimba
......