Fighting Against Hiv/Aids and Sti

Fighting Against Hiv/Aids and Sti

Share

PHUNZILANI ZA HIV/AIDS NDIMATENDA OPATSILANA POGONANA MULI KUNYUMBA. UTHENGA WA CHIPATALA.PANGANI FOLLOW PAGE LATHU.
*ART AND STI CLINICAL MENTOR*

09/10/2026

and mother malawi, ndi mayi malawi, na mama malawi.

09/10/2026

koma nkhani za ititi zimakhala zovuta eeeeee.
kuli ma experience

09/10/2026

Today we will understand why national anthem ndi mawu oti na mama malawi osati dada malawi.

08/10/2026

really appreciate you team for your support and everything zimene mwandichitila lero.
special thanks to the familly amene anatiitana to celebrate with, am back home safely with my dota. Thank you all amene mwatumiza mphatso zotsiyanatsiyana. mwandipasa mphamvu heavy. now will be posting with phaawaa. coz mwaonesa umunthu.

08/10/2026

Morning ife zambiri tilibe tungoti ambuye apitilidze kukudalitsani.
Mwathandiza mwana wanga kuchoka mu depression pano ndimunthu odalilika oro mankhwala akutenga yekha osaopaso anthu.

HBD admin

08/10/2026

Hello admin
Ndinakhala kwa zaka 5 kuopa kulowa mu relationship chifukwa choopa winayo kuti sangandivomele ndi HIV yangayi.
lero takwanisa 8 month in marriage ndi mkaz mnandilumikiza naye uja. Ine nde ndikumva kukoma ndisaname.
As a family we join to celebrate with you on your birthday . tapanga prepare dinner ndife.
HBD enjoy your day

Photos from Fighting Against Hiv/Aids and Sti's post 08/10/2026

poyamba ndinayesa ndi kamkamwa kanatuluka positive nditapita ku chipatala andiyesa katuluka Negative sinduziwa kuti chachitika ndi chani???

answer:
ndizotheka kukhala ndi ma results osalondola ngati sunasate bwino ndondomeko zake. Ndichifukwa timalimbikisa kuti mkaona zotsatila za positive mkuyenela kupita ku chipatala osathamangira kuzikhweza kwanuko. moyo wanu uli ndi phindu kwambiri

08/10/2026

Happy birthday to our own admin and founder of FAHASM MEDICAL CENTER.
pitilizani kuunikila mtundu wa malawi .
Enjoy responsibly osaiwala ngosha as u always say. kkkkkk HBD enjoy your day

07/10/2026

anzanu timaonapo moyo

07/10/2026

Ati wa HIV akamagonana ndikamwana amatenga chitetedzo chambiri safa msanga,
bodza leni leni. pamenepo imakhala kuti maula yikukukodola .

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Telephone

Address

Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Fighting Against Hiv/Aids and Sti posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Subscribe

We will notify you when anything happens in Lilongwe.