TIMO First Class Barbershop
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from TIMO First Class Barbershop, Hair Stylist, Chirimba, Along M1 Road, Lunzu Stage, Blantyre.
Experience the difference in Grooming services, make a statement with your cut!
π Hair Cuts and Styling π Kids Haircut
π Beard Treaming π Hair Styling and Tints
π Facial Scrubs π Pedicure
π Hair conditioningπ Vouchers
Prices on Pinned Post
09/08/2026
Atelotu iwowoooπ
0997 02 91 55
09/08/2026
Eeeh a Madalitso Angel Manyamulah samangoipasa moto chabe Pamudzi pano, akumabwelanso kuzachitila umboni ntchito yabwino Tikupanga! π
Inunso Tipezeni Ku Blantyre Chirimba along M1 Road at Lunzu/Chileka Stage, Pama Truck, Turn Yaku Roman Catholic Church. 0997 02 91 55
Akasi Mukabwela muzangometa, kapena muzafunanso titsuke Mmutu?
π Tipezeni Ku Blantyre Chirimba along M1 Road at Lunzu/Chileka Stage, Pama Truck, Turn Yaku Roman Catholic Church. 0997 02 91 55
09/08/2026
Mwakumbukila Sunday akasi ena analipila ya haircut kuti adalitse ena. Xtina Wa Brown ndi Emmanuel Blessings Botha chisomo chagwela Inu, mukapeza mpata Fikani.
π Tipezeni Ku Blantyre Chirimba along M1 Road at Lunzu/Chileka Stage, Pama Truck, Turn Yaku Roman Catholic Church. 0997 02 91 55
Good morning akasi, Happy Sunday!π
Tipaseni verse yanu yapamtima lero!
08/08/2026
Apa bwanji akasi, zathekatu!π₯ Ma set a clean out of 10 Tichongeni akasi! π
Inunso muzitipeza ku Blantyre Chirimba along M1 Road at Lunzu/Chileka Stage, Pama Truck, Turn Yaku Roman Catholic Church. 0997 02 91 55
Phone number yathu munaisaver kuti chani mu phone mwanumo?
08/08/2026
Zikafika apa mmatani? Titsuke kapena tingozisiya chonchi π¬.
π Visit us today in Blantyre Chirimba along M1 Road at Lunzu /Chileka Stage, Pama Truck, Turn Yaku Roman Catholic Church. 0997 02 91 55
08/08/2026
Akasi kuchita kuchoka ku zalewa! Mzoonadi kuli zabwino sikutalika,. π₯ ifetu akasi Yami Finias mwatilemekeza.
π Inunso Tipezeni Ku Blantyre Chirimba along M1 Road at Lunzu/Chileka Stage, Pama Truck, Turn Yaku Roman Catholic Church.
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Blantyre
Opening Hours
| Monday | 07:00 - 20:00 |
| Tuesday | 07:00 - 20:00 |
| Wednesday | 07:00 - 20:00 |
| Thursday | 07:00 - 20:00 |
| Friday | 07:00 - 20:00 |
| Saturday | 07:00 - 20:00 |
| Sunday | 07:00 - 20:00 |